LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 September tsa. 10
  • October 16-22

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • October 16-22
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 September tsa. 10

October 16-22

YOBU 6-7

  • Nyimbo 33 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Umoyo Ukafika Poti Simungathenso Kupilila”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Yobu 6:29—N’ciyani cingatithandize kupewa kuwaweluza molakwika abale na alongo athu? (w20.04 16 ¶10)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Yobu 6:​1-21 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Mukayamba, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 7)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’gaŵileni cofalitsa ca mu Thuboksi yathu. (th phunzilo 11)

  • Nkhani: (Mph. 5) w22.01 12-13 ¶15-18 Mutu: Muziphunzitsa Mogwila Mtima Monga Yakobo—Muziseŵenzetsa Mafanizo Ogwila Mtima. (th phunzilo 8)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 144

  • “Yehova Amapulumutsa Anthu Odzimvela Cisoni Mumtima Mwawo”: (Mph. 15) Kukambilana na kutamba vidiyo.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff mafunso obweleza a cigawo 4

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nymbo 143 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani