LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 September tsa. 14
  • October 30–November 5

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • October 30–November 5
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 September tsa. 14

October 30–November 5

YOBU 11-12

  • Nyimbo 87 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Njila Zitatu Zopezela Nzelu na Kupindula Nazo”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Yobu 12:11—Kodi mfundo ya pa vesiyi itithandiza bwanji kukulitsa luso la kumvetsela? (w08 8/1 11 ¶5)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Yobu 12:​1-25 (th phunzilo  5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Muuzeni za pulogilamu yathu yophunzitsa Baibo na kum’siyila kakhadi kopemphela phunzilo la Baibo. (th phunzilo 1)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Muitanileni ku misonkhano. Kenako, chulani na kukambilanako vidiyo yakuti N’ciani Cimacitika ku Nyumba ya Ufumu? (Koma musaitambitse.) (th phunzilo 13)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 12 cidule cake, mafunso obweleza, komanso colinga (th phunzilo 19)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 135

  • “Makolo—Thandizani Ana Anu Kupeza Nzelu ya Umulungu”: (Mph. 15) Kukambilana na kutamba vidiyo.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) bt mutu 1 ¶8-15, bokosi pa tsa. 12

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 3 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani