LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 November tsa. 10
  • December 11-17

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • December 11-17
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 November tsa. 10

December 11-17

YOBU 25-27

  • Nyimbo 34 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Tingakhale na Mtima Wosagaŵikana Ngakhale Ndife Opanda Ungwilo”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Yobu 26:14—Kodi zocepa zimene timadziŵako za cilengedwe zimatithandiza kudziŵa ciyani zokhudza Yehova? (w16.11 9 ¶3)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Yobu 25:1–26:14 (th phunzilo 12)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 2) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Mukayamba, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 1)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Onetsani munthuyo mmene angapezele nkhani imene yamucititsa cidwi pa jw.org. (th phunzilo 17)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 13 mawu oyamba na mfundo 1-3 (th phunzilo 15)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 45

  • “Kugwilizana Pakati pa Kusunga Umphumphu na Maganizo Athu”: (Mph. 5) Kukambilana.

  • Zimene Gulu Lakwanitsa Kucita: (Mph. 10) Onetsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Lakwanitsa Kucita ya December.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) bt mutu 3 ¶4-11

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 57 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani