LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 November tsa. 14
  • December 25-31

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • December 25-31
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 November tsa. 14

December 25-31

YOBU 30-31

  • Nyimbo 28 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Zimene Zinathandiza Yobu Kukhalabe Woyela”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Yobu 31:35—Kodi tingapewe bwanji kukhala monga anzake a Yobu ngati wina watiuzako mavuto ake? (w05 11/15 11 ¶3)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Yobu 31:​15-40 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Muuzeni za pulogilamu yathu yophunzitsa Baibo, na kum’patsa kakhadi kopemphela phunzilo la Baibo. (th phunzilo 1)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Itanilani munthuyo ku misonkhano. Chulani na kukambilanako vidiyo yakuti N’ciani Cimacitika ku Nyumba ya Ufumu? (Koma musaitambitse) (th phunzilo 11)

  • Nkhani: (Mph. 5) g16.4 8-9—Mutu: Kodi Ningafotokoze Bwanji Zimene Baibo Imakamba pa Nkhani ya Mathanyula? (th phunzilo 14)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 36

  • “Cifukwa Cake Kuonelela Zamalisece N’koipa”: (Mph. 7) Kukambilana na kutamba vidiyo.

  • Zofunikila za Mpingo: (Mph. 8)

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) bt mutu 4 ¶1-8

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 74 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani