LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb24 September tsa. 4
  • September 9-15

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • September 9-15
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
mwb24 September tsa. 4

SEPTEMBER 9-15

MASALIMO 82-84

Nyimbo 80 na Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Mmodzi wa ana a Kora akuyang’ana cisa ca namzeze mosilila pa bwalo la kacisi

1. Muziyamikila Mwayi wa Utumiki Umene Muli Nawo

(Mph. 10)

Timaukonda kwambili utumiki wathu (Sal. 84:1-3; wp16.6 8 ¶2-3)

Muzisangalala na utumiki umene muli nawo m’malo mongolakalaka umene mulibe (Sal. 84:10; w08-CN 7/15 30 ¶3-4)

Yehova ni wabwino kwa onse amene amam’tumikila mokhulupilika (Sal. 84:11; w20.01 17 ¶12)

Zithunzi: Alevi akugwila nchito zosiyanasiyana. 1. Akuthila madzi m’beseni ya mkuwa poseŵenzetsa mbiya ya dothi. 2. Akukoka ngolo yodzala na mbiya zadothi. 3. Wanyamula mbiya ya dothi.

Utumiki uliwonse uli na madalitso na zovuta zake. Mukamaganizila kwambili pa madalitso, mudzapeza cimwemwe pocita utumiki uliwonse.

2. Kufufuza Cuma Cauzimu

(Mph. 10)

  • Sal. 82:3​—N’cifukwa ciyani kuonetsa cikondi kwa “ana amasiye” mu mpingo n’kofunika? (it-1-E 816)

  • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutifotokozelako?

3. Kuŵelenga Baibo

(Mph. 4) Sal. 82:1–83:18 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

4. Cifundo—Mmene Yesu Anaonetsela Khalidwe Limeneli

(Mph. 7) Kukambilana. Tambitsani VIDIYO, kenako kambilanani lmd phunzilo 9 mfundo 1-2.

5. Cifundo—Tengelani Citsanzo ca Yesu

(Mph. 8) Kukambilana. Seŵenzetsani lmd phunzilo 9 mfundo 3-5 komanso mbali yakuti “Onaninso Malemba Awa.”

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Nyimbo 57

6. Zofunikila za Mpingo

(Mph. 15)

7. Phunzilo la Baibo la Mpingo

(Mph. 30) bt mutu 15 ¶8-12, bokosi pa tsa. 118

Mawu Othela (Mph. 3) | Nyimbo 130 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani