Zina Zimene Zilipo Pa Jw.Org
BAIBULO LIMASINTHA ANTHU
Moyo Wanga Unkangoipilaipilabe
Solomone anali kuganiza kuti akasamukila ku America, azikakhala na umoyo wabwino. M’malo mwake, kumeneko anayamba kugwilitsila nchito mankhwala osokoneza bongo ndipo anamangidwa. Kodi n’ciani cinamuthandiza kuti asinthe umoyo wake?
Pitani pa jw.org ku Chichewa, pa mbali yakuti ZOKHUDZA IFE > ZOCHITIKA PA MOYO WA A MBONI ZA YEHOVA > BAIBULO LIMASINTHA ANTHU.
ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA
Ndingatani Ngati Anzanga Amandiona Kuti Ndine Wotsalila?
Kodi mumaona kuti n’zoyenela kucita zinthu kuti mufanane na anzanu omwe satsatila mfundo za makhalidwe abwino kapena mumaona kuti cofunika ni kungokhala mmene mulili?
Pitani pa jw.org ku Chichewa, pa mbali yakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA > ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA.