Zina Zimene Zilipo Pa Jw.Org
TSANZIRANI CHIKHULUPIRIRO CHAWO
“Sindidzasiya Kukhala Ndi Mtima Wosagawanika”
Kodi nkhani ya Yobu ingatithandize bwanji tikakumana na mavuto kapena mayeselo ena ake amene angayese cikhulupililo cathu?
Pitani pa jw.org ku Chichewa, pa mbali yakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > KUKHULUPIRIRA MULUNGU > TSANZIRANI CHIKHULUPIRIRO CHAWO.
KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?
Luso la Galu Lotha Kununkhiza Zinthu
Kodi cocititsa cidwi na mphuno ya galu n’ciani, zomwenso zacititsa asayansi kufuna kutengela mmene imagwilila nchito, popanga zipangizo zawo?
Pitani pa jw.org ku Chichewa, pa mbali yakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > BAIBULO KOMANSO SAYANSI > KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?