Zina Zimene Zilipo Pa JW.ORG
ZOCHITIKA PA MOYO WA A MBONI ZA YEHOVA
Ankabisa Notsi Pansi pa Mashini Ochapira Zovala
Mayi wina anagwilitsa nchito njila yatsopano pophunzitsa ana ake aakazi mfundo za m’Baibo.
Pitani pa jw.org ku Chichewa, pa mbali yakuti, ZOKHUDZA IFEYO > ZOCHITIKA PA MOYO WA A MBONI ZA YEHOVA > ANAKHALABE OKHULUPIRIKA ATAKUMANA NDI MAYESERO
ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA
Ndingatani Kuti Ndichepetse Thupi?
Mukafuna kucepetsa thupi musamaganize zosiya kudya zakudya zina koma muzisintha mmene mumacitila zinthu pa moyo wanu.
Pitani pa jw.org ku Chichewa, pa mbali yakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA > ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA.