Zina Zimene Zilipo Pa JW.ORG
KALE LATHU
Boti la Lightbearer Linabweretsa Kuwala kwa Choonadi Kum’mwera Chakum’mawa kwa Asia
Ngakhale kuti kagulu kocepa ka oyendetsa boti lakuti Lightbearer anali kutsutsidwa, iwo molimba mtima anafalitsa kuwala kwa coonadi ca m’Baibo m’gawo lalikulu lokhala na anthu ambili.
Pitani pa jw.org, ku Chichewa, pa mbali yakuti LAIBULALE > NKHANI ZOSIYANASIYANA > KALE LATHU.
KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?
Khungu la Kanyama Kooneka Ngati Chipwete
Kodi ni ndani amene anapanga khungu la kanyama ka m’madzi lomwe limasintha mocititsa cidwi?
Pitani pa jw.org, ku Chichewa, pa mbali yakuti LAIBULALE > NKHANI ZOSIYANASIYANA > KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?