Zina Zimene Zilipo Pa JW.ORG
BAIBULO LIMASINTHA ANTHU
N’ciani cinathandiza a Mario amene poyamba anali m’busa kuyamba kukhulupilila kuti Mboni za Yehova zimaphunzitsa coonadi ca m’Baibo?
Pitani pa jw.org, ku Chichewa, pa mbali yakuti LAIBULALE > NKHANI ZOSIYANASIYANA > BAIBULO LIMASINTHA ANTHU.
KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?
Mmene Mano a Nkhono Ina Yam’madzi Anapangidwira
N’ciani cimene cimapangitsa kuti mano a nkhonoyi akhale olimba kwambili kuposa ulusi wa kangaude?
Pitani pa jw.org, ku Chichewa, pa mbali yakuti LAIBULALE > NKHANI ZOSIYANASIYANA > KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?