Zina Zimene Zilipo Pa JW.ORG
KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBULO
Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani Yosamalira Makolo Achikulire?
Baibo imapeleka malangizo othandiza kwa amene amasamalila okalamba.
Pitani pa jw.org, ku Chichewa, pa mbali yakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBULO.
ZOCHITIKA
Ulendo Wokalalikila kwa Anthu Okhala M’phepete mwa Mtsinje wa Maroni
Mboni za Yehova 13 zinanyamuka ulendo wokalalikila uthenga wa m’Baibo wopatsa ciyembekezo, kwa anthu okhala m’madela akutali m’nkhalango ya Amazon ku South America.
Pitani pa jw.org, ku Chichewa, pa mbali yakuti LAIBULALE > NKHANI ZOSIYANASIYANA > ZOCHITIKA PA MOYO WA A MBONI ZA YEHOVA.