Zina Zimene Zilipo Pa JW.ORG
KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBULO
Kodi Tingaphunzire Chiyani kwa Akazi Otchulidwa M’Baibulo?
Onani kusiyana pakati pa akazi ena oopa Mulungu ochulidwa m’Baibo komanso ena amene anali oipa.
Pitani pa jw.org ku Chichewa, pa mbali yakuti, LAIBULALE > NKHANI ZOSIYANASIYANA > KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBULO > BAIBULO.
MMENE ZOPELEKA ZANU ZIMAGWILILA NCHITO
Misonkhano ya Mpingo ya pa Vidiyo Konfalensi
Kodi gulu lathandiza bwanji mipingo kugula ma akaunti a Zoom osakwela mtengo komanso otetezeka kuti izicitila misonkhano pa vidiyo konfalensi?
Pitani pa jw.org pa mbali yakuti, LAIBULALI > MPAMBO WA NKHANI > MMENE ZOPELEKA ZANU ZIMAGWILILA NCHITO.