Zina Zimene Zilipo Pa JW.ORG
MMENE ZOPELEKA ZANU ZIMAGWILILA NCHITO
Kufalitsa Buku Lofunika Kwambili Kuposa Onse
Kumasulila, kupulinta, na kukonza Baibo ya Dziko Latsopano kumaloŵetsamo zambili mwina kuposa zimene munali kudziŵa.
Pitani pa jw.org, pa mbali yakuti LAIBULALI > MPAMBO WA NKHANI > MMENE ZOPELEKA ZANU ZIMAGWILILA NCHITO
BAIBO IMASINTHA ANTHU
“Crime and the Love of Money Brought Me Much Pain”
M’bale Artan atatulutsidwa m’ndende, anaphunzila kuti zimene Baibo imakamba pa nkhani ya kukonda ndalama n’zoona.
Pitani pa jw.org ku Cizungu, pa mbali yakuti LIBRARY > ARTICLE SERIES > THE BIBLE CHANGES LIVES.