Zina Zimene Zilipo Pa JW.ORG
NKHANI ZOKHUDZA MBONI ZA YEHOVA
Tinasankha Kukhala Moyo Wosalira Zambiri
Madián na Marcela anapeza kungokhalila kugula zinthu komanso kukhala na nkhongole yaikulu, kunali kuwonjezela nkhawa mu umoyo wawo. Koma kuphunzitsa ena za Mulungu kunawabweletsela cimwemwe ceniceni.
NKHANI ZINA
Kodi Baibulo Lingakuthandizeni Pakachitika Ngozi Zam’chilengedwe?
Malangizo anzelu a m’Baibo angakuthandizeni ngozi ya zacilengedwe isanacite, ili mkati, komanso pambuyo pake.
MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA
Zimene Makolo Ayenera Kudziwa Zokhudza Kutumiza Mwana Kumalo Osamalira Ana Masana
Makolo asanatumize mwana kumalo osamalila ana masana, ayenela kuganizila ubwino komanso kuipa kwake. Mafunso a m’nkhani ino angakuthandizeni kudziŵa zimene zingathandize mwana wanu.