LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • w23 October masa. 1-32
  • Yophunzila

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yophunzila
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2023
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2023
w23 October masa. 1-32
Angelo kumwamba komanso anthu m’paradaiso pa dziko la pansi, akutamanda Yehova mosangalala.

Yophunzila

OCTOBER 2023

NKHANI ZOPHUNZILA: DECEMBER 11, 2023–JANUARY 7, 2024

© 2023 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika pa dziko lonse lapansi. Nchito imeneyi timaiyendetsa na zopeleka zaufulu. Kuti mupange copeleka, pitani pa donate.jw.org.

Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.

CITHUNZI CA PACIKUTO:

Ganizilani nthawi pamene angelo akumwamba na anthu padziko lapansi adzakhala ogwiIizana pa kumvela kwawo Yehova! (Onani nkhani yophunzila 44, ndime 8)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani