Yophunzila
JUNE 2016
NKHANI ZOPHUNZILA MLUNGU WA: AUGUST 1-28, 2016
© 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
CITHUNZI CA PACIKUTO:
TRINIDAD
M’mbali mwa zilumba za Trinidad ndi Tobago muli midzi yambili imene asodzi amakhalamo. Mboni za Yehova zimalalikila asodzi amene zimapeza kumeneko
OFALITSA
9,679
MAPHUNZILO A BAIBULO
11,331
OPEZEKA PA CIKUMBUTSO (2015)
24,103
Magazini iyi si yogulitsa. Colinga cake ndi kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibulo imene imacitika padziko lonse lapansi. Ndalama zoyendetsela nchitoyi ndi zimene anthu amapeleka mwa kufuna kwao.
Ngati mufuna kupeleka ndalama zocilikizila nchitoyi, pitani pa www.jw.org.
Baibulo limene taseŵenzetsa ndi Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa lina. Komabe, masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lochedwa A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.