Za M’kope Ino
Zipangizo zamakono zingabweletse mavuto amene anthu sangawazindikile.
KODI ZIPANGIZO ZAMAKONO ZIMAKHUDZA BWANJI . . .
Ubwenzi Wanu na Ena?
Ana Anu?
Cikwati Canu?
Luso Lanu Lophunzila Zinthu?
Palibe vidiyo yake.
Pepani, vidiyo yakanga kulila.
Zipangizo zamakono zingabweletse mavuto amene anthu sangawazindikile.
Ubwenzi Wanu na Ena?
Ana Anu?
Cikwati Canu?
Luso Lanu Lophunzila Zinthu?