LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 101
  • Tilalikire Choonadi cha Ufumu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Tilalikire Choonadi cha Ufumu
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Tilalikile Coonadi ca Ufumu
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • “Ku Nyumba ndi Nyumba”
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Khalani ndi Moyo Wopambana
    Imbirani Yehova
  • Umoyo wa Mpainiya
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
Onaninso Zina
Imbirani Yehova
sn nyimbo 101

Nyimbo 101

Tilalikire Choonadi cha Ufumu

(Machitidwe 20:20, 21)

1. Poyamba sitinkadziwa

Zinthu zoti tizichita.

Yehova ’natumiza

Choonadi ndi kuwala.

Ndipo tinazindikira

Chifuniro cha Yehova

Kuti tim’tumikire

Ndi kumalengeza dzina lake.

Timalalikira ndithu

Pamakomo ndi mumsewu

Timathandiza anzathu

Choonadi adziwetu.

Tiyenitu tiyesetse

Mulungu titumikire

Kufikira Yehova

Atanena kuti tamaliza.

(Onaninso Yos. 9:9; Yes. 24:15; Yoh. 8:12, 32.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani