LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 108
  • Cikondi Cokhulupilika ca Mulungu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Cikondi Cokhulupilika ca Mulungu
  • ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Chikondi cha Mulungu N’chosatha
    Imbirani Yehova
  • Kodi Cikondi Cosasintha ca Yehova N’ciani?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2021
  • Cikondi Cokhulupilika Cimam’kondweletsa Yehova—Nanga Imwe?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Tikhale Okhulupilika Nthawi Zonse
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
Onaninso Zina
‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
sjj nyimbo 108

NYIMBO 108

Cikondi Cokhulupilika ca Mulungu

Yopulinta

(Yesaya 55:1-3)

  1. 1. Yehova n’cikondi.

    Anatuma mwana wake.

    Yesu anadzipeleka

    kuti’se timasulidwe.

    Lomba tiyembekezela

    Moyo wosatha padziko.

    (KOLASI)

    Bwelani muphunzile,

    mau opatsa moyo.

    M’lungu afuna kuti

    Mukapeze moyo.

  2. 2. Yehova n’cikondi.

    Nchito zake ni umboni.

    Anaonetsa cikondi,

    Popatsa Yesu Ufumu.

    Ufumuwo unayamba,

    Kulamulila kumwamba.

    (KOLASI)

    Bwelani muphunzile,

    mau opatsa moyo.

    M’lungu afuna kuti

    Mukapeze moyo.

  3. 3. Yehova n’cikondi.

    Na ise tikonde ena.

    Tiŵathandize ofatsa

    Kuti adziŵe Mulungu.

    Tilalikile kwa onse,

    Uthenga wopatsa moyo.

    (KOLASI)

    Bwelani muphunzile,

    mau opatsa moyo.

    M’lungu afuna kuti

    Mukapeze moyo.

(Onaninso Sal. 33:5; 57:10; Aef. 1:7.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani