Pezani Mayankho Pa Mafunso Aya:
Kodi cikondi cimaposa kudziŵa zinthu motani? (1 Akor. 8:1)
Kodi tingaulimbitse bwanji mpingo monga mmene atumiki a Mulungu akale anacitila? (Aroma 13:8)
Kodi tingaonetse bwanji cikondi kwa anthu amene timawalalikila? (1 Ates. 2:7, 8)
Kodi tingathandize bwanji kuti gulu la abale la padziko lonse likule? (Aef. 4:1-3, 11-16; 1 Ates. 5:11)
Kodi tingaonetse bwanji cikondi pa zonse zimene timacita? (1 Akor. 16:14)
© 2019 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania