LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • CO-pgm22 tsa. 8
  • Mawu kwa Osonkhana

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mawu kwa Osonkhana
  • Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2022
  • Nkhani Zofanana
  • Mawu kwa Osonkhana
    Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2021
  • Mawu kwa Osonkhana
    Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2020
  • Mawu kwa Osonkhana
    Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2023
  • Mawu kwa Osonkhana
    Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2024
Onaninso Zina
Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2022
CO-pgm22 tsa. 8

Mawu kwa Osonkhana

Ubatizo Akulu a mpingo wanu anapanga makonzedwe a mmene ubatizo wanu udzacitikila pambuyo pa cigawo ca m’maŵa pa Tsiku Laciŵili.

Zopeleka Msonkhano uno ukumasulidwa m’zinenelo zoposa 500. Zopeleka zanu zaufulu zimathandiza pa nchito ya padziko lonse imeneyi. Mungacite copeleka kupitila pa intaneti mwa kupita pa donate.jw.org. Timayamikila kwambili zopeleka zanu zonse. Bungwe Lolamulila limayamikila ngako kuwolowa manja kwanu kocilikiza zinthu za Ufumu.

Sukulu ya Alengezi a Ufumu

Banja likutsogoza phunzilo la Baibo poseŵenzetsa buku lakuti “Kondwelani na Moyo Kwamuyaya!”

Apainiya a zaka 23 mpaka 65, amene afuna kuwonjezela utumiki wawo, akupemphedwa kuonana na kalembela wa mpingo wawo kuti asaine fomu ya pa intaneti, yofunsila kuloŵa Sukulu ya Alengezi a Ufumu.

Wokonzedwa na Bungwe Lolamulila la Mboni za Yehova

© 2022 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani