Mau oyamba
MUGANIZA BWANJI?
Kodi n’cifunilo ca Mulungu kuti ife anthu tizifa? Baibo imakamba kuti: “[Mulungu] adzapukuta misozi yonse m’maso mwawo, ndipo imfa sidzakhalaponso.”—Chivumbulutso 21:4.
Nsanja ya Mlonda iyi ifotokoza zimene Baibo imakamba pa nkhani ya moyo na imfa.