CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | NEHEMIYA 5–8
Nehemiya anali woyang’anila wa citsanzo cabwino kwambili
Tishiri 455 B.C.E.
8:1-18
Zikuoneka kuti pa cocitikaci, Nehemiya analangiza anthu kusonkhana kuti alambile Mulungu
Anthu anasangalala kwambili
Amuna amene anali mitu ya mabanja, anasonkhana kuti aphunzile zimene zikanawathandiza kutsatila kwambili Cilamulo ca Mulungu
Anthu anakonzekela Cikondwelelo ca Misasa