LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 April tsa. 6
  • Zikumbutso za Msonkhano Wacigawo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Zikumbutso za Msonkhano Wacigawo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Tumitu
  • KODI TINGAONETSE BWANJI CIKONDI . . .
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 April tsa. 6

UMOYO WATHU WACIKRISTU

Zikumbutso za Msonkhano Wacigawo

Nthawi zonse timafuna kuonetsa kuti timakonda Mulungu ndi anzathu pa nthawi ya msonkhano wacigawo. (Mat. 22:37-39) Lemba la 1 Akorinto 13:4-8 limati: “Cikondi n’coleza mtima ndiponso n’cokoma mtima. Cikondi . . . sicicita zosayenela, sicisamala zofuna zake zokha, sicikwiya. . . . Cikondi sicitha.” Conco, pamene muonelela vidiyo ya Zikumbutso za Msonkhano Wacigawo, ganizilani njila zimene mungaonetsele cikondi kwa ena pa msonkhano wacigawo.

KODI TINGAONETSE BWANJI CIKONDI . . .

  • posungila ena malo okhala?

    Banja lakhala pamodzi pa msonkhano wacigawo, ndipo palibe malo amene atsala
  • nyimbo za malimba zikayamba?

    Mboni za Yehova zakhala pansi ndipo zikumvetsela nyimbo za malimba cigawo ca msonkhano cisanayambe
  • pamalo ogona m’dela limene mukucitikila msonkhano?

    Banja lifika pa hotela
  • pogwila nchito yodzifunila?

    Malo ocitilamo msonkhano
    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani