LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 December tsa. 8
  • Kuseŵenzetsa Mphamvu Mwadyela Kumatayitsa Udindo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kuseŵenzetsa Mphamvu Mwadyela Kumatayitsa Udindo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Nkhani Zofanana
  • Cilango Ni Umboni Wakuti Mulungu Amatikonda
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2018
  • Kodi Mudziŵa?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2019
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 December tsa. 8

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | YESAYA 17-23

Kuseŵenzetsa Mphamvu Mwadyela Kumatayitsa Udindo

Sebina anali kapitawo “woyang’anila nyumba” ya mfumu, mwacionekele mfumu Hezekiya. Anali waciŵili kwa mfumu, ndipo anali na udindo waukulu.

Sebina alamula amuna kukonza manda ake

22:15, 16

  • Sebina anayenela kusamalila zosoŵa za anthu a Yehova

  • Koma iye anacita zinthu mwadyela pofuna ulemelelo

22:20-22

  • Yehova anaika Eliyakimu pa udindo wa Sebina

  • Eliyakimu anapatsiwa “makiyi a nyumba ya Davide” amene anaimila mphamvu na ulamulilo

Ganizilani: Kodi Sebina anafunikila kuseŵenzetsa bwanji udindo wake kuti athandize anthu?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani