LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 April tsa. 1
  • Makambilano Acitsanzo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Makambilano Acitsanzo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • ●○○ ULENDO WOYAMBA
  • ○●○ ULENDO WOBWELELAKO WOYAMBA
  • ○○● ULENDO WOBWELELAKO WACIŴILI
  • KAMPENI YOMEMEZA ANTHU KU CIKUMBUTSO (March 23–April 19):
  • Makambilano Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Makambilano Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Makambilano Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • Makambilano Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 April tsa. 1
Banja lilandila munthu ku Cikumbutso

Alandila munthu ku Cikumbutso

Makambilano Acitsanzo

●○○ ULENDO WOYAMBA

Funso: Kodi Yesu anali ndani?

Lemba: Mat. 16:16

Ulalo: N’cifukwa ciani Yesu anafa?

○●○ ULENDO WOBWELELAKO WOYAMBA

Funso: N’cifukwa ciani Yesu anafa?

Lemba: Mat. 20:28

Ulalo: Tingaonetse bwanji kuti timayamikila nsembe ya dipo la Yesu?

○○● ULENDO WOBWELELAKO WACIŴILI

Funso: Tingaonetse bwanji kuti timayamikila nsembe ya dipo la Yesu?

Lemba: Yoh. 17:3

Ulalo: N’ciani cimacitika ku misonkhano ya Mboni za Yehova?

KAMPENI YOMEMEZA ANTHU KU CIKUMBUTSO (March 23–April 19):

Tikuitanilani ku cocitika cofunika kwambili. Kapepa kanu ka ciitanilo ni aka. Pa Cisanu, April 19, anthu mamiliyoni pa dziko lonse, adzasonkhana kuti acite mwambo wokumbukila imfa ya Yesu Khristu. Kapepa ka ciitanilo aka kaonetsa nthawi na malo kumene msonkhanowu udzacitikile kwathu kuno. Tikuitanilaninso ku nkhani imene idzakambidwa kutatsala wiki imodzi cikumbutso cisanacitike. Mutu wake ni wakuti, “Citani Zonse Zotheka Kuti Mukapeze Moyo Weni-Weni!”

Funso la Ulalo Akaonetsa Cidwi: N’cifukwa ciani Yesu anafa?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani