LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 September tsa. 12
  • Tsatilani Yehova na Mtima Wonse

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Tsatilani Yehova na Mtima Wonse
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Azondi 12
    Maphunzilo Amene Tingatengemo m’Baibo
  • Yehova Anawamenyela Nkhondo Aisiraeli
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Malangizo Othela a Yoswa kwa Aisiraeli
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Khalani Wodzicepetsa—Pewani Kudzitamandila
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 September tsa. 12

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Tsatilani Yehova na Mtima Wonse

Kalebe anatsatila Yehova na mtima wonse ali wacinyamata (Yos. 14:7, 8)

Pambuyo pake, Kalebe anadalila Yehova kuti adzamuthandiza kukwanilitsa nchito yovuta (Yos. 14:10-12; w04 12/1 12 ¶2)

Kalebe anadalitsidwa cifukwa cotumikila Yehova na mtima wonse (Yos. 14:13, 14; w06 10/1 18 ¶11)

Zithunzi: Mlongo wokhulupilika akupilila mavuto aukalamba. 1. Wakhala pansi atagwilila ndodo ndipo akupemphela. 2. Akucita ulaliki wapoyela na mlongo wacitsikana. 3. Akuonetsa mapikica ake kwa ana a mumpingo mwawo. 4. Akumwetulila mopanda nkhawa.

Cikhulupililo ca Kalebe cinalimba pamene anali kutsatila malangizo a Yehova na kulandila madalitso ake. Nafenso timalimbikitsidwa kupitiliza kum’tumikila, tikamalandila mayankho pa mapemphelo athu na kuona citsogozo cake m’njila zina zosiyana-siyana.—1 Yoh. 5:14, 15.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani