LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 November tsa. 2
  • Yehova Analigaŵa Mwanzelu Dziko la Kanani

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yehova Analigaŵa Mwanzelu Dziko la Kanani
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Yehova Anawamenyela Nkhondo Aisiraeli
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Tetezani Coloŵa Canu Camtengo Wapatali
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Malangizo Othela a Yoswa kwa Aisiraeli
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Yehova Amapatula Anthu Ake
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 November tsa. 2
Zithunzi: 1. Pamene watsala pang’ono kumwalila, Yakobo akukambilatu zimene zidzacitikila ana ake. 2. Mapu a Dziko Lolonjezedwa oonetsa mmene malo anagaŵidwila kwa mafuko 12 a Isiraeli.

Yakobo akukambilatu zimene zidzacitikila ana ake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova Analigaŵa Mwanzelu Dziko la Kanani

Yehova anapeleka citsogozo poseŵenzetsa maele, mwina pofuna kuonetsa kumene fuko lililonse la Isiraeli linayenela kulandila colowa cawo ca malo (Yos. 18:10; it-1 359 ¶1)

Yehova anaonetsetsa kuti ulosi umene Yakobo anapeleka pa nthawi ya kufa kwake wakwanilitsidwa (Yos. 19:1; it-1 1200 ¶1)

Yehova anapatsa Aisiraeli udindo woona kukula kwa malo amene fuko lililonse linayenela kulandila (Yos. 19:9; it-1 359 ¶2)

Dzikolo linagaŵidwa m’njila imene inathandiza kuti mafuko a Isiraeli asamacitilane nsanje kapena kulimbilana malo. Kodi zimenezi zakuthandizani kukhala na cidalilo cotani na mmene Yehova adzayendetsela zinthu m’dziko latsopano?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani