CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Yehova Ni Mulungu Woganizila Ena
Samueli anaganiza kuti Eli anali kumuitana (1 Sam. 3:4-7; w18.09 24 ¶3)
Yehova anaonetselatu kuti iye ndiye anali kuitana Samueli (1 Sam. 3:8, 9)
Yehova anacita zinthu mom’ganizila Samueli wacicepeleyo (1 Sam. 3:15-18; w18.09 24 ¶4)
DZIFUNSENI KUTI: ‘Ningaonetse bwanji kuti nimawaganizila acicepele komanso acikulile? Ningaonetse bwanji kuti nimaganizila ena pa misonkhano yacikhristu?