LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 July tsa. 2
  • Barizilai Ni Citsanzo ca Kudzicepetsa

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Barizilai Ni Citsanzo ca Kudzicepetsa
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Akhristu Acikulile Yehova Amayamikila Kukhulupilika Kwanu
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2018
  • Mukhoza Kukhalabe Wodzicepetsa Ngakhale pa Ciyeso
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2017
  • N’cifukwa Ciani Kudzicepetsa N’kofunikabe?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2017
  • Malangizo Othela a Yoswa kwa Aisiraeli
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 July tsa. 2
Barizilai akukana mwayi umene Mfumu Davide yam’patsa.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Barizilai Ni Citsanzo ca Kudzicepetsa

Barizilai anapatsidwa mwayi wapadela na Mfumu Davide (2 Sam. 19:32, 33; w07 7/15 14 ¶5)

Cifukwa ca kudzicepetsa, Barizilai anakana mwaulemu mwayi umene anapatsidwa (2 Sam. 19:34, 35; w07 7/15 14 ¶7)

Khalani odzicepetsa monga Barizilai (w07 7/15 15 ¶1-2)

Kudzicepetsa kumatithandiza kuzindikila zimene sitingakwanitse kucita. Tiyenela kukhala odzicepetsa kuti tikondweletse Yehova. (Mika 6:8) Kodi timapindula bwanji tikamaonetsa khalidwe la kudzicepetsa?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani