LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 September tsa. 9
  • Kodi Mukayika-kayika Mpaka Liti?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kodi Mukayika-kayika Mpaka Liti?
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Muziyang’ana kwa Yehova Kuti Mupeze Citonthozo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Citsanzo Cimene Tingatengele pa Nkhani ya Kulankhulana Bwino
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Kodi Mumaugwila Mtima?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Asa Anacita Zinthu Molimba Mtima—Kodi Inunso Mumatelo?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 September tsa. 9
Eliya, aneneli a Baala, na ena akuona pamene moto ukutsika kucokela kumwamba na kunyeketsa nsembe yopseleza pa guwa la nsembe.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Mukayika-kayika Mpaka Liti?

Eliya anauza Aisiraeli kuti sanafunike kukayika-kayika popanga cisankho (1 Maf. 18:21; w17.03 14 ¶6)

Baala anali mulungu wopanda moyo (1 Maf. 18:25-29; ia 88 ¶15)

Yehova anadzionetsa kuti ni Mulungu woona mwa kucita cozizwitsa (1 Maf. 18:36-38; ia 90 ¶18)

Eliya anauza anthuwo kuti aonetse cikhulupililo cawo mwa kumvela Cilamulo ca Yehova. (Deut. 13:5-10; 1 Maf. 18:40) Masiku anonso, timaonetsa kuti tili na cikhulupililo komanso ndife odzipeleka kwa Yehova mwa kutsatila malamulo ake mosamala.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani