CITANI KHAMA PA ULALIKI
Makambilano Acitsanzo
Kampeni Yoyambitsa Maphunzilo a Baibo (September 1-30)
Funso: Kodi n’zotheka kukapeza moyo wamuyaya wacisangalalo?
Lemba: Sal. 37:29
Ulalo: Kodi tingakhulupililedi zimene Baibo imalonjeza?
Ulendo Woyamba
Funso: N’kuti kumene tingapeze malangizo othandiza pa umoyo?
Lemba: 2 Tim. 3:16, 17
Ulalo: N’cifukwa ciyani muyenela kuikhulupilila Baibo?
Ulendo Wobwelelako
Funso: N’cifukwa ciyani muyenela kuikhulupilila Baibo?
Lemba: Yobu 26:7
Ulalo: Kodi ni mafunso ena ati amene Baibo imayankha?