LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 March tsa. 2
  • Kulambila pa Kacisi Kunayamba Kucitika Mwadongosolo Kwambili

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kulambila pa Kacisi Kunayamba Kucitika Mwadongosolo Kwambili
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Utumiki wa Alevi
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Mfundo Zothandiza Kuweluza Milandu Mwacilungamo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Mmene Cilamulo Cinaonetsela Kuti Yehova Amadela Nkhawa Osauka
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Zimene Tingaphunzile pa Dongosolo la Msasa wa Aisiraeli
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 March tsa. 2

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kulambila pa Kacisi Kunayamba Kucitika Mwadongosolo Kwambili

Mfumu Davide anagaŵa Alevi na ansembe m’magulu-magulu kuti azigwila nchito za pakacisi (1 Mbiri 23:6, 27, 28; 24:1, 3; it-2 241, 686)

Akatswili oimba komanso anthu ena ophunzila kuimba anapatsidwa utumiki woimba nyimbo (1 Mbiri 25:1, 8; it-2 451-452)

Alevi anaikidwa kukhala alonda a pazipata, amsungacuma, komanso ogwila nchito zina (1 Mbiri 26:16-20; it-1 898)

Abale na alongo msonkhano wa mpingo usanayambe. 1. Alongo akupatsana moni na kuceza. 2. M’bale akuonetsa mlongo zina zake zimene zinaikidwa pa notisibodi. 3. Mlongo akuponya zopeleka m’bokosi la zopeleka. 4. M’bale amene ali pamalo otengela mabuku akupatsa mlongo mabuku. 5. M’bale akukonza maikolofoni ku pulatifomu. 6. M’bale na mwana wake wacicepele akuyeletsa.

Timalambila Yehova mwadongosolo cifukwa iye ni wadongosolo.—1 Akor. 14:33.

ZOYENELA KUZISINKHASINKHA: N’ciyani cionetsa kuti mpingo wacikhristu umacita zinthu mwadogosolo polambila Yehova masiku ano?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani