LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 March tsa. 6
  • “Mtima Wanga Udzakhala Pamenepa Nthawi Zonse”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • “Mtima Wanga Udzakhala Pamenepa Nthawi Zonse”
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • “Khulupililani Yehova Mulungu Wanu”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Pindulani na Ulangizi Wanzelu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Anagwila Nchito Molimbika Cifukwa Cokonda Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Kodi Mumapindula Nawo Mofikapo Mawu a Mulungu?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 March tsa. 6

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Mtima Wanga Udzakhala Pamenepa Nthawi Zonse”

Yehova anadzisankhila yekha kacisi (2 Mbiri 7:11, 12)

Yehova anati nthawi zonse mtima wake udzakhala pa kacisiyo, kuonetsa kuti adzakhala na cidwi coona zimene zikucitika pa nyumbayo, imene inali kudziŵika na dzina lake (2 Mbiri 7:16; w02 11/15 5 ¶1)

Mulungu anati Aisiraeli akadzaleka kuyenda pamaso pake “ndi mtima wawo wonse,” iye adzalola kuti kacisiyo awonongedwe (2 Mbiri 6:14; 7:19-21; it-2 1077-1078)

Zithunzi: Zocita zokhudza kulambila. 1. M’bale akupemphela. 2. Mlongo akupeleka ndemanga pa msonkhano wa mpingo. 3. Mwamuna na mkazi wake akulalikila capamodzi. 4. M’bale akuyeletsa Nyumba ya Ufumu. 5. M’bale akucititsa kulambila kwa pabanja ali na mkazi wake komanso ana awo aŵili. 6. Mlongo akuŵelenga Baibo. 7. Mlongo akuponya zopeleka m’bokosi la zopeleka.

Pa nthawi yopatulila kacisi, mwina anthuwo anali kuganiza kuti mitima yawo idzakhalabe pa kacisiyo nthawi zonse. Koma n’zacisoni kuti pang’ono-m’pang’ono, cangu cawo polambila Yehova cinacepa.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi nimaonetsa bwanji kuti nimaika mtima wanga wonse pa kulambila?’

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani