LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsa. 6
  • Yehova Amadalitsa Anthu Ocita Zinthu Molimba Mtima

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yehova Amadalitsa Anthu Ocita Zinthu Molimba Mtima
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • N’cifukwa Ciyani Tiyenela Kumuopa Yehova?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2023
  • Yehoyada Anali Wolimba Mtima
    Maphunzilo Amene Tingatengemo m’Baibo
  • Kutumikila Yehova Sikovuta
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Kodi Mumapindula Nawo Mofikapo Mawu a Mulungu?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 May tsa. 6
Zithunzi: 1. Yehoyada na Yehosabati, mwakacetecete atenga Yehoasi wakhanda kuti akamubise. 2. Mkulu wa ansembe Yehoyada akuveka Yehoasi wacicepele cisoti cacifumu pomulonga ufumu.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova Amadalitsa Anthu Ocita Zinthu Molimba Mtima

Yehosabati na mwamuna wake Yehoyada, anateteza Yehoasi kwa Ataliya. (2 Mbiri 22:11, 12; w09 4/1 24 ¶1-2)

Molimba mtima, Yehoyada anaika Yehoasi kukhala mfumu (2 Mbiri 23:1-11, 14, 15; w09 4/1 24 ¶3-5)

Yehoyada atamwalila anapatsidwa ulemu wapadela woikidwa m’manda a mafumu (2 Mbiri 24:15, 16; it-1 379 ¶5)

ZOYENELA KUSINKHASINKHA: Ni pa mbali ziti za kulambila kwathu pamene niyenela kuonetsa kulimba mtima kwambili?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani