CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Musawasiye Konse Alambili Anzanu
Acibale a Yobu analeka kuyanjana naye (Yobu 19:13)
Ngakhale ana aang’ono komanso anchito ake analeka kumulemekeza (Yobu 19:16, 18)
Ngakhalenso mabwenzi ake apamtima anamuukila (Yobu 19:19)
DZIFUNSENI KUTI, Ningaonetse bwanji kuti nimaŵakonda abale na alongo amene akukumana na mavuto?—Miy. 17:17; w22.01 16 ¶9; w21.09 30 ¶16; w90 9/1 22 ¶20.