Mawu Amunsi
b Ngakhale ziŵanda nthawi zina zimamvela, koma mokakamizika. Pamene Yesu analamula ziŵanda kuti zituluke mwa anthu, izo zinakakamizika kuzindikila ulamulilo wake ndi kumumvela monyinyilika.—Maliko 1:27; 5:7-13.