Mawu Amunsi a Liu la Ciheberi lotembenuzidwa kuti “cinyengo” pa Miyambo 15:4 lingatanthauzenso “kupotoka.”