Mawu Amunsi
c Iwo anali kugwilitsila nchito sikelo ina pogula ndi ina pogulitsa ndi colinga cakuti apeze phindu loculuka. Anali kugwilitsilanso nchito sikelo ya ndodo yaitali kapena yolema kwambili mbali imodzi, ndi colinga cakuti azibela anthu.