Mawu Amunsi
a Maina ofotokoza zocita za Satana (monga akuti Wotsutsa, Woneneza, Wonyenga, Woyesa, Wabodza) satanthauza kuti iye amadziŵa zimene zili mumtima ndi m’maganizo athu. Koma mosiyana ndi Satana, Yehova amafotokozedwa kuti “amayesa mitima,” ndipo Yesu ‘amafufuza impso ndi mitima.’—Miyambo 17:3; Chivumbulutso 2:23.