Mawu Amunsi
a Pofuna kupewa kugwilitsila nchito kompyuta mosayenelela, mabanja ambili amaika kompyuta yao pa malo oonekela kwa onse m’nyumba. Ndiponso, mabanja ena amagula mapulogalamu a pakompyuta amene amapangitsa kuti zinthu zoipa zisaloŵe mu kompyuta yao. Komabe, mapulogalamu a pakompyuta ndi osadalilika kwenikweni.