Mawu Amunsi
b Kuti mudziŵe njila zina zothandiza za mmene mungathetsele vuto loseŵeletsa malisece, onani nkhani yakuti “Zimene Achinyamata Amadzifunsa . . . Kodi Ndingathetse Bwanji Cizolowezi Cimeneci?” mu Galamukani! ya November 2006 ndi buku la Cingelezi lakuti Young People Ask—Answers That Work, Volume 1 patsamba 178 mpaka 182.