Mawu Amunsi
b Mabuku ena amene athandiza ofalitsa kuphunzitsa anthu Baibulo ndi awa: Zeze wa Mulungu (lofalitsidwa mu 1921), “Mulungu Akhale Oona” (lofalitsidwa mu 1946), Mungathe Kukhala ndi Moyo Kosatha (lofalitsidwa mu 1982), ndi Chidziŵitso Chotsogolera ku Moyo Wosatha (lofalitsidwa mu 1995).