Mawu Amunsi
a Yesu ananena mau akuti ‘minda yayela kale,’ mwina ataona mikanjo yoyela imene gulu la a Samariya anavala. Gulu limenelo linali kubwela kwa iye.