Mawu Amunsi
b Kuti mudziŵe zambili ponena za zimene zinacitika pa zakazo ndiponso zaka zina zambili pambuyo pake, tikukulimbikitsani kuŵelenga buku lacingelezi lakuti Jehovah’s Witnesses—Proclaimers of God’s Kingdom, patsamba 425 mpaka 520. Bukuli limalongosola zimene nchito yokolola inakwanilitsa kuyambila mu 1919 mpaka mu 1992.