Mawu Amunsi
d Ophunzila Baibulo anali kudziŵa kale coonadi cofunika kwambili cimeneci. Magazini ya Zion’s Watch Tower ya November 15, 1895, inati: “Ngakhale kuti tingasonkhanitse tiligu wocepa, umboni woculuka ndi wamphamvu umakhala kuti wapelekedwa. . . . Anthu onse angalalikile uthenga wabwino.”