Mawu Amunsi c Nkhani imeneyi inafotokoza kuti deti la m’nyengo yozizila limene anthu ena amati ndi pamene Yesu anabadwa, siligwilizana ndi nkhani ya m’Baibulo imene imafotokoza kuti abusa anali kunja usiku ndi ziweto zao. —Luka 2:8.