Mawu Amunsi
d Kalata imene M’bale Frederick W. Franz analemba pa November 14, 1927 inati: “Caka cino sitidzakhala ndi Krisimasi. Banja la Beteli lagamula kuti tisamacite Krisimasi.” Pambuyo pa miyezi ingapo, M’bale Franz analembanso kalata ina. M’kalatayo iye anati: “Ambuye pang’onopang’ono akutiyeletsa kucoka ku zodetsa za Mdyelekezi zimene zili m’machalichi a Babulo.”