Mawu Amunsi
a Mlandu wa m’bale Cantwell unali woyamba pa milandu 43 ya ku Khoti lalikulu ku United States imene M’bale Hayden Covington anakamba poteteza abale. M’bale Covington anamwalila mu 1978. Mkazi wake, Dorothy, anatumikila mokhulupilika mpaka pamene anamwalila mu 2015 ali ndi zaka 92.