Mawu Amunsi
b Ciweluzoci cinazikidwa pa lamulo limene linakhazikitsidwa mu 1606. Lamulo limenelo linapeleka mphamvu kwa oweluza kuti azim’patsa mlandu munthu ngati aona kuti zimene munthuyo anakamba ndi zoyambitsa mkangano ngakhale kuti anakamba zoona.